Nehemiya 8:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mawa mwace akuru a nyumba za makolo a anthu onse, ansembe, ndi Alevi anasonkhana pamodzi kwa Ezara mlembi, kuti atole nzeru za mau a cilamulo.

Nehemiya 8

Nehemiya 8:12-14