Nehemiya 7:70 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ena a akuru a nyumba za makolo anapereka kunchito. Kazembeyo anapereka kucuma madariki agolidi cikwi cimodzi, mbale zawazira makumi asanu, maraya a ansembe makumi atatu.

Nehemiya 7

Nehemiya 7:66-73