Nehemiya 7:61 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo okwera kucokera ku Telemela, Teleharisa, Kerubi, Adoni, ndi Imeri, ndi awa; koma sanakhoza kuchula nyumba za makolo ao, kapena mbumba zao, ngati ali a Israyeli;

Nehemiya 7

Nehemiya 7:54-69