Nehemiya 6:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiponso waika aneneri akubukitsa za iwe ku Yerusalemu, ndi kuti, Ku Yuda kuli mfumu, ndipo zidzamveka kwa mfumu, kuti kuli zotere. Tiyeni tsono tipangane pamodzi.

Nehemiya 6

Nehemiya 6:1-11