Nehemiya 6:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mukumbukile, Mulungu wanga, Tobiya ndi Sanibalati monga mwa nchito zao izi, ndi Nowadiya mneneri wamkazi yemwe, ndi aneneri otsala, amene anafuna kundiopsa.

Nehemiya 6

Nehemiya 6:9-19