Nehemiya 6:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kunali tsono, atamva Sanibalati, ndi Tobiya, ndi Gesemu M-arabu, ndi adani athu otsala, kuti ndidatha kumanga lingali, posatsalaponso popasuka; (ngakhale pajapo sindinaika zitseko pazipata);

Nehemiya 6

Nehemiya 6:1-9