Nehemiya 5:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma akazembe akale ndisanakhale ine, analemetsa anthu, nadzitengera kwa iwo mkate, ndi vinyo, pamodzi ndi siliva masekeli makumi anai; angakale anyamata ao anacita ufumu pa anthu; koma sindinatero ine, cifukwa ca kuopa Mulungu.

Nehemiya 5

Nehemiya 5:9-19