Nehemiya 4:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo musakwirira mphulupulu yao, ndi kulakwa kwao kusafafanizike pamaso panu; pakuti anautsa mkwiyo wanu pamaso pa omanga linga.

Nehemiya 4

Nehemiya 4:3-9