Nehemiya 4:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nanena iye pamaso pa abale ace ndi ankhondo a ku Samariya, nati, Alikucitanji Ayuda ofokawa? adzimangire linga kodi? adzapereka nsembe kodi? adzatsiriza tsiku limodzi kodi? adzakometsanso miyala ya ku miunda yotenthedwa?

Nehemiya 4

Nehemiya 4:1-7