Nehemiya 3:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi cipata cakale anacikonza Yoyada mwana wa Paseya; ndi Mesulamu mwana wa Besodeya anamanga mitanda yace, ndi kuika zitseko zace, ndi zokowera zace, ndi mipingiridzo yace.

Nehemiya 3

Nehemiya 3:4-16