Nehemiya 3:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potsatizana nao anakonza Zadoki mwana wa Imeri pandunji pa nyumba yace. Ndi potsatizana naye anakonza Semaya mwana wa Sekaniya, wosunga cipata ca kum'mawa.

Nehemiya 3

Nehemiya 3:21-32