Nehemiya 3:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Palali mwana wa Uzai anakonza pandunji popindirira, ndi nsanja yosomphoka pa nyumba ya mfumu ya kumtunda, imene iri ku bwalo la kaidi. Potsatizana naye anakonza Pedaya mwana wa Parosi.

Nehemiya 3

Nehemiya 3:18-30