Nehemiya 3:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potsatizana nao anakonza Benjamini ndi Hasubi pandunji pa nyumba pao, Potsatizana nao anakonza Azariya mwana wa Maseya mwana wa Ananiya pafupi pa nyumba yace.

Nehemiya 3

Nehemiya 3:14-32