Nehemiya 3:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi pa mbali pace Ezeri mwana wa Yesuwa, mkuru wa Mizipa, anakonza gawo lina, pandunji pokwerera ku nyumba yosungamo zida za nkhondo, popindirira linga.

Nehemiya 3

Nehemiya 3:9-29