Nehemiya 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potsatizana naye anakonza Alevi, Rehumu mwana wa Bani. Pambali pace anakonza Hasabiya mkuru wa dera lina la dziko la Keila, kukonzera dziko lace.

Nehemiya 3

Nehemiya 3:12-27