Nehemiya 3:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi pambali pao anakonza Yedaya mwana wa Harumafi, pandunji pa nyumba yace. Ndi pambali pace anakonza Hatusi mwana wa Hasabineya.

Nehemiya 3

Nehemiya 3:8-16