Nehemiya 2:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma olamulira sanadziwa uko ndinamuka, kapena cocita ine; sindidauzenso kufikira pamenepo Ayuda, kapena ansembe, kapena aufuru, kapena olamulira, kapena otsala akucita nchitoyi.

Nehemiya 2

Nehemiya 2:6-20