Nehemiya 13:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo ndinafika ku Yerusalemu, ndi kuzindikira coipa anacicita Eliasibu, cifukwa ca Tobiya, ndi kumkonzera cipinda m'mabwalo a nyumba ya Mulungu.

Nehemiya 13

Nehemiya 13:2-15