Nehemiya 13:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma wina wa ana a Yoyada, mwana wa Eliasibu mkuru wa ansembe, anali mkamwini wa Sanibalati Mhoroni; cifukwa cace ndinampitikitsa kumcotsa kwa ine.

Nehemiya 13

Nehemiya 13:23-31