Nehemiya 12:46 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti m'masiku a Davide ndi Asafu kalelo kunali mkuru wa oyimbira, ndi wa nyimbo zolemekeza ndi zoyamikira Mulungu.

Nehemiya 12

Nehemiya 12:45-47