Nehemiya 12:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atatero, magulu awiriwo a iwo oyamikira anaima m'nyumba ya Mulungu, ndipo ine ndi limodzi la magawo awiri a olamulira pamodzi ndi ine;

Nehemiya 12

Nehemiya 12:35-46