Nehemiya 12:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi ku cipata ca kucitsime, ndi kundunji kwao, anakwerera pa makwerero a mudzi wa Davide, potundumuka linga, popitirira pa nyumba ya Davide, mpaka ku cipata ca kumadzi kum'mawa.

Nehemiya 12

Nehemiya 12:27-38