Nehemiya 12:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ndinakwera nao akuru a Yuda pa lingali, ndinaikanso oyamikira magulu awiri akuru oyenda molongosoka; lina loyenda ku dzanja lamanja palinga kumka ku cipata ca kudzala;

Nehemiya 12

Nehemiya 12:25-38