Nehemiya 12:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi akuru a Alevi: Hasabiya, Serebiya, ndi Yesuwa mwana wa Kadimiyeli, ndi abale ao openyana nao, kulemekeza ndi kuyamika, monga mwa lamulo la Davide munthu wa Mulungu, alonda kupenyana alonda.

Nehemiya 12

Nehemiya 12:17-28