Nehemiya 12:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

M'masiku a Ehasibi, Yoyada, Yohanana, ndi Yoduwa, Alevi analembedwa akuru a nyumba za makolo; ansembe omwe, mpaka ufumu wa Dariyo wa ku Perisiya.

Nehemiya 12

Nehemiya 12:15-26