Nehemiya 12:2-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

2. Amariya, Maluki, Hatusi,

3. Sekaniya, Rehumu, Meremoti,

4. Ido, Ginetoi, Abiya,

5. Miyamini, Maadiya, Biliga,

6. Semaya, ndi Yoyaribi, Yedaya,

7. Salu, Amoki, Hilikiya, Yedaya. Awa ndi akuru a ansembe ndi abale ao m'masiku a Yesuwa.

8. Ndi Alevi ndiwo Yesuwa, Binui, Kadimiyeli, Serebiya, Yuda, ndi Mataniya; iye ndi abale ace amatsogolera mayamiko.

Nehemiya 12