Nehemiya 11:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi ana a Benjamini ndi awa: Salu mwana wa Mesulamu, mwana wa Yoedi, mwana wa Pedaya, mwana Wa Kolaya, mwana wa Maseya, mwana wa Itiyeli, mwana wa Yesaya.

Nehemiya 11

Nehemiya 11:2-11