Nehemiya 11:27-30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

27. ndi m'Hazarisuala, ndi m'Beereseba ndi miraga yace,

28. ndi m'Zikilaga, ndi m'Mekona ndi miraga yace,

29. ndi m'Enirimoni, ndi m'Zora, ndi m'Yarimuti,

30. Zanowa, Adulamu ndi midzi yao, Lakisi ndi minda yace, Azeka ndi miraga yace. Ndipo anamanga misasa kuyambira ku Beereseba mpaka cigwa ca Hinomu.

Nehemiya 11