Nehemiya 1:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakumva'mau awa, ndinakhala pansi ndi kulira misozi, ndi kucita maliro masiku ena, ndinasalanso, ndi kupemphera pamaso pa Mulungu wa Kumwamba,

Nehemiya 1

Nehemiya 1:1-9