Nehemiya 1:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

anafika Hanani, mmodzi wa abale anga, iye ndi amuna ena a ku Yuda; ndipo ndinawafunsa za Ayuda adapulumukawo otsala andende, ndi za Yerusalemu.

Nehemiya 1

Nehemiya 1:1-5