Nahumu 3:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Abusa ako aodzera, mfumu ya ku Asuri; omveka ako apumula; anthu ako amwazika pamapiri, ndipo palibe wakuwasonkhanitsa.

Nahumu 3

Nahumu 3:14-19