Nahumu 3:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Tsoka mudzi wa mwazi! udzala nao mabodza ndi zacifwamba; zacifwamba sizidukiza.

2. Kumveka kwa cikoti, ndi mkokomo wa kuyenda kwa njinga za magareta; ndi kaphata kaphata wa akavalo, ndi gwegwegwe wa magareta;

Nahumu 3