Nahumu 1:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova: Angakhale iwo ali ndi mphamvu yokwanira, nacuruka momwemo, koma momwemonso adzasalikidwa, ndipo iye adzapitiratu. Cinkana ndakuzunza iwe, sindidzakuzunzanso.

Nahumu 1

Nahumu 1:3-15