Mlaliki 8:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo ndinaona nchito zonse za Mulungu kuti anthu sangalondole nchito ziciddwa pansi pano; pakuti angakhale munthu ayesetsa kuzifunafuna koma sadzazipeza; indetu ngakhalenso wanzeru akati, ndidziwa, koma adzalephera kuzilondola.

Mlaliki 8

Mlaliki 8:10-17