Mlaliki 8:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pompo ndinatama kusekaseka, pakuti munthu alibe kanthu kabwino pansi pano, koma kudya ndi kumwa, ndi kusekera; ndi kuti zimenezi zikhalebe naye m'bvuto lace masiku onse a moyo wace umene Mulungu wampatsa pansi pano.

Mlaliki 8

Mlaliki 8:10-17