Mlaliki 8:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinaona oipa alikuikidwa m'manda ndi kupita; ndipo omwe anacita zolungama anacokera ku malo opatulika a ku mudzi nawaiwala; icinso ndi cabe.

Mlaliki 8

Mlaliki 8:7-14