Mlaliki 7:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Tsiku la mwai kondwera, koma tsiku la tsoka lingirira; Mulungu waika ici pambali pa cinzace, kuti anthu asapeze kanthu ka m'tsogolo mwao.

Mlaliki 7

Mlaliki 7:9-19