Mlaliki 5:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usalole m'kamwa mwako mucimwitse thupi lako; usanene pamaso pa mthenga kuti, Ndinaphophonya; Mulungu akwiyire mau ako cifukwa ninji, naononge nchito ya manja ako?

Mlaliki 5

Mlaliki 5:1-9