Mlaliki 5:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inde yemwe Mulungu wamlemeretsa nampatsa cuma, namninkhanso mphamvu ya kudyapo, ndi kulandira gawo lace ndi kukondwera ndi nchito zace; umenewu ndiwo mtulo wa Mulungu.

Mlaliki 5

Mlaliki 5:14-20