Mlaliki 2:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndani adziwa ngati adzakhala wanzeru pena citsiru? Koma adzalamulira nchito zanga zonse ndinasauka nazo, ndi kuzigwira mwanzeru kunja kuno. Icinso ndi cabe.

Mlaliki 2

Mlaliki 2:9-22