Mlaliki 11:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Inde, munthu akakhala ndi moyo zaka zambiri, akondwere ndi zonsezo; koma akumbukire masiku amdima kuti adzacuruka. Zonse zirinkudza ziri zacabe.

Mlaliki 11

Mlaliki 11:3-10