Mlaliki 10:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Usatemberere mfumu ngakhale poganizira; usatemberere wolemera m'cipinda cogona iwemo; pakuti mbalame ya mlengalenga idzanyamula mauwo, ndipo couluka ndi mapiko cidzamveketsa zonenazo.

Mlaliki 10

Mlaliki 10:10-20