Mlaliki 1:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinalankhula ndi mtima wanga, ndi kuti, Taona, ndakuza ndi kudzienjezera nzeru koposa onse anakhala m'Yerusalemu ndisanabadwe ine; inde mtima wanga wapenyera kwambiri nzeru ndi cidziwitso.

Mlaliki 1

Mlaliki 1:11-18