Mlaliki 1:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndinapereka mtima kufunafuna ndi nzeru, ndi kulondetsa zonse zimacitidwa pansi pa thambo; nchito yobvuta imeneyi Mulungu apatsa ana a anthu akasauke nayo.

Mlaliki 1

Mlaliki 1:5-18