Miyambi 8:1-4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Kodi nzeru siitana,Luntha ndi kukweza mau ace?

2. Iima pamwamba pa mtunda,Pa mphambano za makwalala;

3. Pambali pa cipata polowera m'mudzi,Polowa anthu pa makomo ipfuula:

4. Ndinu ndikuitanani, amuna,Mau anga ndilankhula kwa ana a anthu.

Miyambi 8