Miyambi 6:32-35 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

32. Wocita cigololo ndi mkazi alibe nzeru;Wofuna kuononga moyo wace wace ndiye amatero.

33. Adzalasidwa nanyozedwa;Citonzo cace sicidzafafanizidwa.

34. Pakuti nsanje ndiyo ukali wa mwamuna,Ndipo sadzacitira cifundo tsiku lobwezera cilango.

35. Sadzalabadira ciombolo ciri conse,Sadzapembedzeka ngakhale ucurukitsa malipo,

Miyambi 6