Miyambi 31:14-17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Akunga zombo za malonda;Nakatenga zakudya zace kutari.

15. Aukanso kusanace,Napatsa banja lace zakudya, nagawira adzakazi ace nchito.

16. Asinkhasinkha za munda, naugula;Naoka mipesa ndi zipatso za manja ace.

17. Amanga m'cuuno mwace ndi mphamvu,Nalimbitsa mikono yace,

Miyambi 31