Miyambi 30:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndingakhute ndi kukukanani, ndi kuti, Yehova ndani?Kapena ndingasauke ndi kuba,Ndi kuchula dzina la Mulungu wanga pacabe.

Miyambi 30

Miyambi 30:1-15