Miyambi 30:32-33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

32. Ngati wapusa podzikweza,Ngakhale kuganizira zoipa, tagwira pakamwa.

33. Pakuti potakasa mkaka, mafuta ayengekapo;Ndi popsinja mpfuno, mwazi uturukamo;Ndi potimbikira mkwiyo ndeu ionekamo.

Miyambi 30