Miyambi 30:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Mau a Aguri mwana wa Yake; uthenga. Munthuyo anati, Ndadzitopetsa, Mulungu;Ndadzitopetsa, Mulungu, ndathedwa;